3 Koma akalonga a ana a Amoni anauza Hanuni kuti: “Kodi mukuganiza kuti Davide watumiza anthu odzakutonthozani kuti alemekeze bambo anu pamaso panu? Kodi atumiki akewa sanabwere kwa inu kuti adzaonetsetse mzindawu ndi kuchita ukazitape,+ kuti adzaulande?”+