1 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anakabwereka magaleta 32,000 ndiponso kulemba ganyu mfumu ya ku Maaka ndi anthu ake. Zitatero, iwo anabwera nʼkumanga misasa yawo pafupi ndi Medeba.+ Aamoni anatuluka mʼmizinda yawo nʼkusonkhana kuti akamenye nkhondo.
7 Choncho anakabwereka magaleta 32,000 ndiponso kulemba ganyu mfumu ya ku Maaka ndi anthu ake. Zitatero, iwo anabwera nʼkumanga misasa yawo pafupi ndi Medeba.+ Aamoni anatuluka mʼmizinda yawo nʼkusonkhana kuti akamenye nkhondo.