1 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero anakabwereka magaleta 32,000,+ ndi kulemba ganyu mfumu ya ku Maaka ndi anthu ake.+ Zitatero, iwowa anafika ndi kumanga misasa yawo pafupi ndi Medeba.+ Ndipo ana a Amoni anatuluka m’mizinda yawo ndi kusonkhana kuti akamenye nkhondo.
7 Chotero anakabwereka magaleta 32,000,+ ndi kulemba ganyu mfumu ya ku Maaka ndi anthu ake.+ Zitatero, iwowa anafika ndi kumanga misasa yawo pafupi ndi Medeba.+ Ndipo ana a Amoni anatuluka m’mizinda yawo ndi kusonkhana kuti akamenye nkhondo.