-
1 Mbiri 19:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Aamoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa Abisai mchimwene wake wa Yowabu nʼkupita mumzinda. Kenako Yowabu anabwerera ku Yerusalemu.
-