1 Mbiri 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Amoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa+ pamaso pa Abisai m’bale wake ndi kubwerera kumzinda.+ Kenako Yowabu anabwerera ku Yerusalemu.
15 Ana a Amoni ataona kuti Asiriya athawa, nawonso anathawa+ pamaso pa Abisai m’bale wake ndi kubwerera kumzinda.+ Kenako Yowabu anabwerera ku Yerusalemu.