1 Mbiri 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Davide nʼkuyamba kumutumikira.+ Asiriya sanafunenso kuthandiza Aamoni.
19 Atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Davide nʼkuyamba kumutumikira.+ Asiriya sanafunenso kuthandiza Aamoni.