1 Mbiri 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonja pamaso pa Isiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Davide n’kuyamba kumutumikira.+ Asiriya sanayesenso kupulumutsa ana a Amoni.+
19 Atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonja pamaso pa Isiraeli,+ nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Davide n’kuyamba kumutumikira.+ Asiriya sanayesenso kupulumutsa ana a Amoni.+