Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+ Salimo 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Inu mudzandiveka mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo.Mudzakomola ondiukira.+
7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+