1 Mbiri 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero Davide anatchuka+ mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse. Ndipo Yehova anachititsa kuti mitundu yonse iziopa Davide.+ Salimo 18:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anthu akangomva mphekesera chabe zokhudza ine, adzandimvera.+Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+
17 Chotero Davide anatchuka+ mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse. Ndipo Yehova anachititsa kuti mitundu yonse iziopa Davide.+
44 Anthu akangomva mphekesera chabe zokhudza ine, adzandimvera.+Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+