1 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma mfumu inakana kumvera zimene Yowabu ananena. Choncho Yowabu ananyamuka ndipo anayenda mu Isiraeli monse. Kenako anabwerera ku Yerusalemu.+
4 Koma mfumu inakana kumvera zimene Yowabu ananena. Choncho Yowabu ananyamuka ndipo anayenda mu Isiraeli monse. Kenako anabwerera ku Yerusalemu.+