1 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma mawu a mfumu+ anaposa mawu a Yowabu moti Yowabu anachoka pamaso pa mfumu+ n’kuyenda mu Isiraeli yense. Kenako anabwerera ku Yerusalemu.+
4 Koma mawu a mfumu+ anaposa mawu a Yowabu moti Yowabu anachoka pamaso pa mfumu+ n’kuyenda mu Isiraeli yense. Kenako anabwerera ku Yerusalemu.+