2 Samueli 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamapeto pake mawu a mfumu anaposa+ mawu a Yowabu ndi atsogoleri a magulu ankhondo. Choncho Yowabu ndi atsogoleri a magulu ankhondowo anachoka pamaso pa mfumu ndi kupita kukawerenga+ anthu a Isiraeli.
4 Pamapeto pake mawu a mfumu anaposa+ mawu a Yowabu ndi atsogoleri a magulu ankhondo. Choncho Yowabu ndi atsogoleri a magulu ankhondowo anachoka pamaso pa mfumu ndi kupita kukawerenga+ anthu a Isiraeli.