1 Mbiri 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yowabu sanawerenge anthu a fuko la Levi ndi la Benjamini,+ chifukwa mawu a mfumu anamunyansa kwambiri.+
6 Koma Yowabu sanawerenge anthu a fuko la Levi ndi la Benjamini,+ chifukwa mawu a mfumu anamunyansa kwambiri.+