-
1 Mbiri 21:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Davide atafika kwa Orinani, Orinani nʼkumuona Davideyo, nthawi yomweyo anachoka pamalo opunthira mbewu aja nʼkugwada pamaso pa Davide ndipo anawerama mpaka nkhope yake kufika pansi.
-