1 Mbiri 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Davide uja anakafika kwa Orinani. Ndiye Orinani atakweza maso n’kuona Davide,+ nthawi yomweyo anachoka pamalo opunthira mbewu aja n’kukagwada pamaso pa Davide n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.
21 Davide uja anakafika kwa Orinani. Ndiye Orinani atakweza maso n’kuona Davide,+ nthawi yomweyo anachoka pamalo opunthira mbewu aja n’kukagwada pamaso pa Davide n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.