2 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Arauna atasuzumira panja anaona mfumu ndi atumiki ake akubwera kwa iye. Nthawi yomweyo Arauna anatuluka ndi kugwada+ pamaso pa mfumu ndipo anawerama mpaka nkhope yake pansi.+
20 Arauna atasuzumira panja anaona mfumu ndi atumiki ake akubwera kwa iye. Nthawi yomweyo Arauna anatuluka ndi kugwada+ pamaso pa mfumu ndipo anawerama mpaka nkhope yake pansi.+