-
1 Mbiri 21:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma Orinani anauza Davide kuti: “Ingotengani malowa kwaulere ndipo mbuyanga mfumu chitani chilichonse chimene mukuona kuti nʼchabwino. Ineyo ndipereka ngʼombe kuti zikhale nsembe zopsereza ndi chopunthira tirigu+ kuti chikhale nkhuni ndiponso ndipereka tirigu kuti akhale nsembe yambewu. Ndikupereka zonsezi.”
-