1 Mbiri 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumbali ya mbadwa za Izara,+ panali Kenaniya ndi ana ake omwe anali akapitawo ndi oweruza+ Isiraeli, koma ntchito yawoyi ankagwirira kunja kwa nyumba ya Mulungu.
29 Kumbali ya mbadwa za Izara,+ panali Kenaniya ndi ana ake omwe anali akapitawo ndi oweruza+ Isiraeli, koma ntchito yawoyi ankagwirira kunja kwa nyumba ya Mulungu.