1 Mbiri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yasobeamu anali mbadwa ya Perezi.+ Iye anali mkulu wa atsogoleri onse a magulu amene ankatumikira mwezi woyamba.
3 Yasobeamu anali mbadwa ya Perezi.+ Iye anali mkulu wa atsogoleri onse a magulu amene ankatumikira mwezi woyamba.