1 Mbiri 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yowabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize. Ndipo Mulungu anakwiyira kwambiri Aisiraeli chifukwa chowerenga anthuwo,+ moti chiwerengerocho sichinalembedwe mʼmbiri ya zochitika za nthawi ya Mfumu Davide.
24 Yowabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize. Ndipo Mulungu anakwiyira kwambiri Aisiraeli chifukwa chowerenga anthuwo,+ moti chiwerengerocho sichinalembedwe mʼmbiri ya zochitika za nthawi ya Mfumu Davide.