-
1 Mbiri 27:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Simeyi wa ku Rama anali woyangʼanira minda ya mpesa koma Zabidi wa ku Sifimi anali woyangʼanira zinthu zonse zokhudza vinyo zamʼminda ya mpesayo.
-