1 Mbiri 27:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Simeyi wa ku Rama anali woyang’anira minda ya mpesa,+ koma Zabidi wa ku Sifimi anali woyang’anira zinthu zonse zokhudza vinyo za m’minda ya mpesayo.
27 Simeyi wa ku Rama anali woyang’anira minda ya mpesa,+ koma Zabidi wa ku Sifimi anali woyang’anira zinthu zonse zokhudza vinyo za m’minda ya mpesayo.