1 Mbiri 27:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Baala-hanani wa ku Gederi anali woyangʼanira mitengo ya maolivi ndi ya mkuyu+ imene inali ku Sefela+ ndipo Yowasi ankayangʼanira mafuta.
28 Baala-hanani wa ku Gederi anali woyangʼanira mitengo ya maolivi ndi ya mkuyu+ imene inali ku Sefela+ ndipo Yowasi ankayangʼanira mafuta.