1 Mbiri 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chuma ndi ulemerero zimachokera kwa inu.+ Inu mumalamulira chilichonse.+ Mʼdzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+
12 Chuma ndi ulemerero zimachokera kwa inu.+ Inu mumalamulira chilichonse.+ Mʼdzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+