-
2 Mbiri 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Phiko limodzi la kerubi winayo linali lalitali mikono 5 ndipo linagunda khoma lina la chipindacho. Phiko lina linalinso lalitali mikono 5 ndipo linakagunda phiko la kerubi woyamba uja.
-