2 Mbiri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Phiko limodzi la kerubi wina linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho, ndipo phiko linalo, lalitali mikono isanu, linali kukhudzana ndi phiko la kerubi mnzake.+
12 Phiko limodzi la kerubi wina linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho, ndipo phiko linalo, lalitali mikono isanu, linali kukhudzana ndi phiko la kerubi mnzake.+