Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kerubi wachiwiri anali wotalika mikono 10. Akerubi awiriwo anali ofanana kukula kwawo ndiponso kapangidwe kawo.

  • 1 Mafumu 6:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako anaika akerubiwo m’chipinda chamkati, ndipo mapiko awo anali otambasula.+ Nsonga ya phiko la kerubi mmodzi inagunda khoma ndipo nsonga ya phiko la kerubi winayo inagundanso khoma lina. Mapiko awo anafika pakati pa nyumbayo, ndipo anagundana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena