Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 80:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+

      Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+

      Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+

  • Yesaya 37:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Inu Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi, inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Aheberi 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena