2 Mbiri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Phiko limodzi la kerubi wina linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho, ndipo phiko linalo, lalitali mikono isanu, linali kukhudzana ndi phiko la kerubi mnzake.+ 2 Mbiri 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mapiko a akerubiwo anali otambasukira pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba+ pa Likasa ndi pamwamba pa mitengo yake yonyamulira.+
12 Phiko limodzi la kerubi wina linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho, ndipo phiko linalo, lalitali mikono isanu, linali kukhudzana ndi phiko la kerubi mnzake.+
8 Mapiko a akerubiwo anali otambasukira pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba+ pa Likasa ndi pamwamba pa mitengo yake yonyamulira.+