1 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akerubiwo anatambasulira mapiko awo pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasa ndi mitengo yake yonyamulira.+
7 Akerubiwo anatambasulira mapiko awo pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasa ndi mitengo yake yonyamulira.+