Ekisodo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro. Ekisodo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapiko a akerubiwo anali okweza m’mwamba ndi otambasula.+ Iwo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo anakhala moyang’anizana, koma nkhope zawo zinayang’ana pachivundikirocho.+ 2 Mbiri 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mapiko a akerubiwo anali otambasukira pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba+ pa Likasa ndi pamwamba pa mitengo yake yonyamulira.+
20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro.
9 Mapiko a akerubiwo anali okweza m’mwamba ndi otambasula.+ Iwo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo anakhala moyang’anizana, koma nkhope zawo zinayang’ana pachivundikirocho.+
8 Mapiko a akerubiwo anali otambasukira pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba+ pa Likasa ndi pamwamba pa mitengo yake yonyamulira.+