1 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akerubiwo anatambasulira mapiko awo pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasa ndi mitengo yake yonyamulira.+ 1 Mbiri 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anayezanso golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ malinga ndi kulemera kwake, ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.
7 Akerubiwo anatambasulira mapiko awo pamwamba pa malo okhala Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasa ndi mitengo yake yonyamulira.+
18 Anayezanso golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ malinga ndi kulemera kwake, ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.