Ekisodo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro. 1 Samueli 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+ 1 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, m’chipinda chamkati anapangamo akerubi+ awiri kuchokera ku mtengo wamafuta.* Kerubi aliyense anali mikono 10 kutalika kwake.+ Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro.
4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+
23 Komanso, m’chipinda chamkati anapangamo akerubi+ awiri kuchokera ku mtengo wamafuta.* Kerubi aliyense anali mikono 10 kutalika kwake.+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+