Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.

  • 2 Mafumu 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ pamaso pa Yehova, kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse+ a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba+ ndi dziko lapansi.+

  • 2 Mbiri 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 M’chipinda cha Malo Oyera Koposa anapangamo zifaniziro za akerubi+ ziwiri n’kuzikuta ndi golide.+

  • Salimo 99:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 99 Yehova wakhala mfumu.+ Mitundu ya anthu inthunthumire.+

      Iye wakhala pa akerubi.+ Ndipo dziko lapansi linjenjemere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena