Ekisodo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapiko a akerubi awiriwo anawakweza mʼmwamba nʼkuwatambasula ndipo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo.+ Akerubiwo anakhala moyangʼanizana ndipo nkhope zawo zinaweramira pachivundikirocho.+
9 Mapiko a akerubi awiriwo anawakweza mʼmwamba nʼkuwatambasula ndipo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo.+ Akerubiwo anakhala moyangʼanizana ndipo nkhope zawo zinaweramira pachivundikirocho.+