Ekisodo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapiko a akerubiwo anali okweza m’mwamba ndi otambasula.+ Iwo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo anakhala moyang’anizana, koma nkhope zawo zinayang’ana pachivundikirocho.+
9 Mapiko a akerubiwo anali okweza m’mwamba ndi otambasula.+ Iwo anaphimba chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo anakhala moyang’anizana, koma nkhope zawo zinayang’ana pachivundikirocho.+