Genesis 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo. Ekisodo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro. Aheberi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.
24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.
20 Ndipo akweze mapiko awo m’mwamba ali otambasula, aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo, ndipo akhale moyang’anizana,+ koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro.
5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.