2 Mbiri 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Hiramu,+ kudzera mwa antchito ake, ankatumizira Solomo zombo ndi antchito odziwa zapanyanja. Ulendo uliwonse umene iwo limodzi ndi antchito a Solomo apita ku Ofiri,+ ankabweretsera Mfumu Solomo+ golide wokwana matalente* 450.+
18 Hiramu,+ kudzera mwa antchito ake, ankatumizira Solomo zombo ndi antchito odziwa zapanyanja. Ulendo uliwonse umene iwo limodzi ndi antchito a Solomo apita ku Ofiri,+ ankabweretsera Mfumu Solomo+ golide wokwana matalente* 450.+