2 Mbiri 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Hiramu,+ kudzera mwa antchito ake, ankatumizira Solomo zombo ndi antchito odziwa za panyanja.+ Iwo ankapita ku Ofiri+ pamodzi ndi antchito a Solomo kukatenga golide+ wokwana matalente* 450,+ ndipo anali kubwera naye kwa Mfumu Solomo.+
18 Hiramu,+ kudzera mwa antchito ake, ankatumizira Solomo zombo ndi antchito odziwa za panyanja.+ Iwo ankapita ku Ofiri+ pamodzi ndi antchito a Solomo kukatenga golide+ wokwana matalente* 450,+ ndipo anali kubwera naye kwa Mfumu Solomo.+