Mlaliki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinapezanso siliva ndi golide wambiri,+ ndi chuma chimene chimakhala ndi mafumu ndiponso chimene chimapezeka m’zigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi.+ Ndinalinso ndi akazi ambiri,+ omwe amasangalatsa mtima+ wa amuna.
8 Ndinapezanso siliva ndi golide wambiri,+ ndi chuma chimene chimakhala ndi mafumu ndiponso chimene chimapezeka m’zigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi.+ Ndinalinso ndi akazi ambiri,+ omwe amasangalatsa mtima+ wa amuna.