1 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo. Nyimbo ya Solomo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakati pa mafumukazi 60, adzakazi* 80 ndi atsikana osawerengeka,+
3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.