2 Mbiri 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Alevi ndi Ayuda onse anachitadi zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga asilikali ake amene ankagwira ntchito pa Sabata ndi amene ankafunika kupuma pa Sabata,+ popeza wansembe Yehoyada sanawauze kuti azipita.+
8 Alevi ndi Ayuda onse anachitadi zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga asilikali ake amene ankagwira ntchito pa Sabata ndi amene ankafunika kupuma pa Sabata,+ popeza wansembe Yehoyada sanawauze kuti azipita.+