2 Mbiri 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anthu onse anapita kukachisi wa Baala nʼkukamugwetsa+ ndipo anaphwanyaphwanya maguwa ndi mafano ake.+ Anaphanso wansembe wa Baala+ dzina lake Mateni kutsogolo kwa maguwa ansembewo.
17 Kenako anthu onse anapita kukachisi wa Baala nʼkukamugwetsa+ ndipo anaphwanyaphwanya maguwa ndi mafano ake.+ Anaphanso wansembe wa Baala+ dzina lake Mateni kutsogolo kwa maguwa ansembewo.