Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+

  • 2 Mbiri 34:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yosiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 8 ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu.+

  • 2 Mbiri 34:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kuwonjezera pamenepo, anthu anagwetsa maguwa ansembe a Abaala pamaso pake, ndipo iye anagumula zofukizira zimene zinali pamwamba pa maguwawo. Mizati yopatulika,* zifaniziro zogoba ndi zifaniziro zachitsulo, anaziphwanya nʼkuziperapera. Fumbi lake analiwaza pamanda a anthu amene ankapereka nsembe kwa zinthu zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena