2 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehoasi anayamba kulamulira ali ndi zaka 7.+ Iye analamulira zaka 40 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Beere-seba ndipo dzina lawo linali Zibiya.+
24 Yehoasi anayamba kulamulira ali ndi zaka 7.+ Iye analamulira zaka 40 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Beere-seba ndipo dzina lawo linali Zibiya.+