-
2 Mbiri 24:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno mfumuyo inaitana mtsogoleri wawo Yehoyada nʼkumufunsa kuti:+ “Bwanji simunauze Alevi kuti abweretse msonkho wopatulika kuchokera kwa anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu? Si paja anayenera kubweretsa msonkho wopatulika wochokera kwa Aisiraeli wogwiritsa ntchito pachihema cha Umboni+ womwe Mose+ mtumiki wa Yehova analamula?
-