2 Mbiri 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu amene anamʼkonzera chiwembuwo+ ndi awa: Zabadi yemwe mayi ake anali Simeyati, mbadwa ya Amoni, ndiponso Yehozabadi yemwe mayi ake anali Simiriti, wa ku Mowabu.
26 Anthu amene anamʼkonzera chiwembuwo+ ndi awa: Zabadi yemwe mayi ake anali Simeyati, mbadwa ya Amoni, ndiponso Yehozabadi yemwe mayi ake anali Simiriti, wa ku Mowabu.