2 Mbiri 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uziya anapitiriza kufunafuna Mulungu mʼmasiku a Zekariya yemwe ankamuphunzitsa kuti aziopa Mulungu woona. Pa nthawi imene iye ankafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:5 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 10
5 Uziya anapitiriza kufunafuna Mulungu mʼmasiku a Zekariya yemwe ankamuphunzitsa kuti aziopa Mulungu woona. Pa nthawi imene iye ankafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+