2 Mbiri 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uziya anali kufunafuna+ Mulungu m’masiku a Zekariya yemwe anali kumulangiza kuti aziopa Mulungu woona.+ M’masiku amene iye anafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:5 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 10
5 Uziya anali kufunafuna+ Mulungu m’masiku a Zekariya yemwe anali kumulangiza kuti aziopa Mulungu woona.+ M’masiku amene iye anafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+