2 Mbiri 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene ankatulutsa ndalama zimene zinabwera kunyumba ya Yehova,+ wansembe Hilikiya anapeza buku la Chilamulo cha Yehova+ loperekedwa kudzera mwa Mose.+
14 Pamene ankatulutsa ndalama zimene zinabwera kunyumba ya Yehova,+ wansembe Hilikiya anapeza buku la Chilamulo cha Yehova+ loperekedwa kudzera mwa Mose.+